Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 20:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Yehova anati kwa Yoswa,

2. Nena ndi ana a Israyeli ndi kuti, Mudziikire midzi yopulumukirako, monga ndinanena kwa inu mwa dzanja la Mose,

3. kuti athawireko wakupha munthu osamupha dala, osadziwa; ndipo idzakhalira inu yopulumukirako, kumpulumuka wolipsa mwazi.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 20