Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 19:51 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Izi ndizo zolowa anazigawa Eleazare wansembe, ndi Yoswa mwana wa Nuni, ndi akulu a nyumba za atate a mapfuko a ana a Israyeli, zikhale zao zao, ndi kulota maere ku Silo pamaso pa Yehova ku khomo la cihema cokomanako. Momwemo anatha kuligawa dziko.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 19

Onani Yoswa 19:51 nkhani