Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 19:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma malire a ana a Dani anaturuka kupitirira iwowa; pakuti ana a Dani anakwera nathira nkhondo ku Lesemu, naulanda naukantha ndi lupanga lakuthwa, naulandira, nakhala m'mwemo, naucha Lesemu, Dani; ndilo dzina la Dani atate wao.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 19

Onani Yoswa 19:47 nkhani