Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 18:22-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. ndi Beti-araba, ndi Zemaraimu, ndi Beteli;

23. ndi Arimu ndi Para, ndi Ofira;

24. ndi Kefaraamoni, ndi Ofini, ndi Geba; midzi khumi ndi iwiri pamodzi ndi miraga yao;

25. Gibeoni ndi Rama, ndi Beeroti;

26. ndi Mizipe, ndi Kefira, ndi Moza;

27. ndi Rekemu, ndi Iripeeli ndi Tarala;

Werengani mutu wathunthu Yoswa 18