Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 18:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi Zela, Elefi, ndi Yebusi, womwewo ndi Yerusalemu, Gibeati ndi Kiriyati; midzi khumi ndi inai pamodzi ndi miraga yace, Ndico colowa ca ana a Benjamini monga mwa mabanja ao.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 18

Onani Yoswa 18:28 nkhani