Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 17:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa ananena kwa iwo a m'nyumba ya Yosefe, kwa Efraimu ndi Manase, ndi kuti, Inu ndinu anthu aunyinji, muli nayo mphamvu yaikuru; simudzakhala nalo gawo limodzi lokha;

Werengani mutu wathunthu Yoswa 17

Onani Yoswa 17:17 nkhani