Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 15:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo analemba malire kuyambira pamwamba pa phiri mpaka citsime ca madzi ca Nefitoa, naturukira malire ku midzi ya phiri la Efroni; ndipo analemba malire kumka ku Baala, ndiwo Kiriyati-Yearimu.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 15

Onani Yoswa 15:9 nkhani