Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 15:63 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ana a Yuda sanakhoza kuingitsa Ayebusi, nzika za Yerusalemu: m'mwemo Ayebusi anakhala pamodzi ndi ana a Yuda, ku Yerusalemu, mpaka lero lino.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 15

Onani Yoswa 15:63 nkhani