Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 15:54-58 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

54. ndi Humita, ndi Kiriyatiariba, ndiwo Hebroni, ndi Ziori; midzi isanu ndi inai pamodzi ndi miraga yao.

55. Maoni, Karimeli, ndi Zifu, ndi Yuta;

56. ndi Yesireeli, ndi Yokideamu, ndi Zoona;

57. Kaini, Gibea ndi Timina; midzi khumi pamodzi ndi miraga yao.

58. Haluli, Beti-zuru, ndi Gedori,

Werengani mutu wathunthu Yoswa 15