Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 15:38-42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

38. ndi Dilani, ndi Mizipe, ndi Yokiteeli;

39. Lakisi ndi Bozikatu ndi Egiloni;

40. ndi Kaboni, ndi Lamasi, ndi, Kitilisi;

41. ndi Gaderotu, Beti-dagoni, ndi Naama, ndi Makeda; midzi khumi ndi isanu ndi umodzi pamodzi ndi miraga yao.

42. Libina ndi Eteri ndi Asana;

Werengani mutu wathunthu Yoswa 15