Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 15:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Mundipatse dalitso; popeza mwandipatsa dziko la kumwela, ndipatseninso zitsime za madzi. Pamenepo anampatsa zitsime za kumtunda, ndi zitsime za kunsi.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 15

Onani Yoswa 15:19 nkhani