Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 14:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose analumbira tsiku lomwelo ndi kuti, Zedi, dzikoli phazi lako lapondapo lidzakhala colowa cako, ndi ca ana ako kosalekeza, cifukwa unatsata Yehova Mulungu wanga ndi mtima wonse.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 14

Onani Yoswa 14:9 nkhani