Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 14:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, taonani, Yehova anandisunga ndi moyo, monga ananena, zaka izi mak umi anai ndi zisanu kuyambira nthawi ija Yehova ananena kwa Mose mau awa, poyenda Israyeli m'cipululu; ndipo tsopano taonani, ndine wa zaka makumi asanu ndi atatu, kudza zisanu lero lino.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 14

Onani Yoswa 14:10 nkhani