Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 14:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Hebroni likhala colowa cace ca Kalebe mwana wa Yefune Mkenizi mpaka lero lino; popeza anatsata Yehova Mulungu wa Israyeli ndi mtima wonse.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 14

Onani Yoswa 14:14 nkhani