Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 14:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, ndipatseni phiri ili limene Yehova ananenera tsiku lija; pakuti udamva tsiku lijalo kuti Aanaki anali komweko, ndi midzi yaikuru ndi yamalinga; kapena Yehova adzakhala ndi ine, kuti ndiwaingitse monga ananena Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 14

Onani Yoswa 14:12 nkhani