Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 13:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamodzi ndi iye Arubeni ndi Agadi analandira colowa cao, cimene Mose adawapatsa tsidya ilo la Yordano kum'mawa, monga Mose mtumiki wa Yehova anawapatsa;

Werengani mutu wathunthu Yoswa 13

Onani Yoswa 13:8 nkhani