Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 13:32-33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

32. Izi ndi zolowazi Mose anazigawira m'zidikha za Moabu, tsidya ilo la Yordano ku Yeriko, kum'mawa.

33. Koma pfuko la Levi, Mose analibe kulipatsa colowa: Yehova Mulungu wa lsrayeli, ndiye colowa cao, monga ananena nao.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 13