Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 13:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi Gileadi logawika pakati, ndi Asitarotu ndi Edrei, midzi ya ufumu wa Ogi m'Basana, inali ya ana a Makiri mwana wa Manase, ndiwo ana a Makiri ogawika pakati, monga mwa mabanja ao.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 13

Onani Yoswa 13:31 nkhani