Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 12:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mose mtumiki wa Yehova ndi ana a Israyeli anawakantha; ndi Mose mtumiki wa Yehova analipereka kwa Arubeni, ndi Agadi ndi pfuko la Manase logawika pakati, likhale colowacao.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 12

Onani Yoswa 12:6 nkhani