Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 1:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komatu khala wamphamvu, nulimbike mtima kwambiri, kuti usamalire kucita monga mwa cilamulo conse anakulamuliraco Mose mtumiki wanga; usacipambukire ku dzanja lamanja kapena kulamanzere, kuti ukacite mwanzeru kuli konse umukako.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 1

Onani Yoswa 1:7 nkhani