Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 1:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akazi anu, ana anu, ndi zoweta zanu zikhale m'dzikoli anakuninkhani Mose, tsidya lino la Yordano; koma inu muoloke okonzeka kunkhondo pamaso pa abale anu, ngwazi zonse, ndi kuwathandiza;

Werengani mutu wathunthu Yoswa 1

Onani Yoswa 1:14 nkhani