Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yona 4:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo sindiyenera Ine kodi kucitira cifundo Nineve mudzi waukuru uwu; m'mene muli anthu oposa zikwi zana limodzi mphambu zikwi makumi awiri osadziwa kusiyanitsa pakati pa dzanja lao lamanja ndi lamanzere, ndi zoweta zambiri zomwe?

Werengani mutu wathunthu Yona 4

Onani Yona 4:11 nkhani