Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yona 4:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati, Unacitira cifundo msatsiwo umene sunagwirapo nchito, kapena kuumeretsa, umene unamera usiku, nutha usiku;

Werengani mutu wathunthu Yona 4

Onani Yona 4:10 nkhani