Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 35:14-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Inde mungakhale munena, Sindimpenya,Mlanduwo uli pamaso pace, ndipo mumlindira.

15. Ndipo tsopano popeza analibe kumzonda m'kukwiya kwace,Ndi kusamalitsa colakwa,

16. Cifukwa cace Yobu anatsegula pakamwa pace mwacabe,Nacurukitsa mau opanda nzeru.

Werengani mutu wathunthu Yobu 35