Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 23:14-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Pakuti adzacita condiikidwiratu;Ndipo zambiri zotere ziri ndi Iye.

15. Cifukwa cace ndiopsedwa pankhope pace;Ndikalingirira, ndicita mantha ndi Iye.

16. Pakuti Mulungu walefula mtima wanga,Ndi Wamphamvuyonse wandiopsa.

Werengani mutu wathunthu Yobu 23