Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 16:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo Yobu anayankha, nati,

2. Ndamva zambiri zotere;Inu nonse ndinu otonthoza mtima mondilemetsa.

3. Kodi adzatha mau ouluzika?Kapena cikuwindula nciani kuti uyankha zotere?

4. Inenso ndikadanena monga inu,Moyo wanu ukadakhala m'malo mwa moyo wanga,Ndikadalumikizanitsa mau akutsutsana nanu,Ndi kukupukusirani mutu wanga.

Werengani mutu wathunthu Yobu 16