Inenso ndikadanena monga inu,Moyo wanu ukadakhala m'malo mwa moyo wanga,Ndikadalumikizanitsa mau akutsutsana nanu,Ndi kukupukusirani mutu wanga.