Popeza masiku ace alembedwa, ciwerengo ca miyezi yace cikhala ndi Inu,Ndipo mwamlembera malire ace, kuti asapitirirepo iye;