Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 14:20-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Mumlaka cilakire, napita iye;Musintha nkhope yace, mumuuza acoke.

21. Ana ace aona ulemu osadziwa iye;Napeputsidwa, koma osazindikira za iwo.

22. Koma thupi lace limuwawira yekha,Ndi mtima wace umliritsa yekha.

Werengani mutu wathunthu Yobu 14