Dziko la mdima bii ngati mdima wandiweyani,Dziko la mthunzi wa imfa losalongosoka,Kumene kuunika kukunga mdima.