Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 10:21-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Ndisanacoke kumka kumene sindikabweranso,Ku dziko la mdima ndi la mthunzi wa imfa;

22. Dziko la mdima bii ngati mdima wandiweyani,Dziko la mthunzi wa imfa losalongosoka,Kumene kuunika kukunga mdima.

Werengani mutu wathunthu Yobu 10