Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 9:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Ambuye sadzakondwera ndi anyamata ao, ngakhale kuwacitira cifundo amasiye ao ana ndi akazi; popeza yense ali wodetsa ndi wocimwa, m'kamwa monse mulankhula zopusa. Mwa izi zonse mkwiyo wace sunacoke, koma dzanja lace liri citambasulire.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 9

Onani Yesaya 9:17 nkhani