Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 9:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti iwo amene atsogolera anthuwa, ndiwo awasokeretsa; ndipo iwo amene atsogoleredwa nao aonongeka.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 9

Onani Yesaya 9:16 nkhani