Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 8:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace, taonani, Ambuye atengera pa iwo madzi a Nyanja, olimba ndi ambiri, kunena mfumu ya Asuri ndi ulemerero wace wonse; ndipo iye adzadzala mphaluka zace zonse, nadzasefukira pamtunda ponse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 8

Onani Yesaya 8:7 nkhani