Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 8:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza anthu awa akana madzi a Silowa, amene ayenda pang'ono pang'ono, nakondwerera mwa Rezini ndi mwa mwana wa Remaliya;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 8

Onani Yesaya 8:6 nkhani