Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 8:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Yehova anati kwa ine, Tenga iwe polembapo papakuru, nulembe pamenepo ndi malembedwe odziwika, Kangazakufunkha Fulumirakusakaza,

2. Ndipo ndidzadzitengera ine mboni zokhulupirika, Uriya wansembe, ndi Zekariya mwana wa Yeberekiya.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 8