Ndipo ndinanka kwa mneneri wamkazi; ndipo iye anatenga pakati nabala mwana wamwamuna. Ndipo Yehova anati kwa ine, Uche dzina lace, Kangazakufunkha Fulumirakusakaza.