Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 7:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali masiku a Ahazi, mwana wa Yotamu, mwana wa Uziya, mfumu ya Yuda, kuti Rezini, mfumu ya Aramu, ndi Peka, mwana wa Remaliya, mfumu ya Israyeli, anakwera kunka ku Yerusalemu, kumenyana nao; koma sanathe kuupamnana.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 7

Onani Yesaya 7:1 nkhani