Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 66:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndani anamva kanthu kotereko? ndani anaona zinthu zoterezo? Kodi dziko lidzabadwa tsiku limodzi? Kodi mtundu udzabadwa modzidzimutsa? pakuti pamene Ziyoni anamva zowawa, pomwepo anabala ana ace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 66

Onani Yesaya 66:8 nkhani