Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 66:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau a phokoso acokera m'mudzi, mau ocokera m'Kacisi, mau a Yehova amene abwezera adani ace cilango.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 66

Onani Yesaya 66:6 nkhani