Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 65:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo sadzamanga, ndi wina kukhalamo; iwo sadzanka, ndi wina kudya; pakuti monga masiku a mtengo adzakhalamasiku a anthu anga; ndi osankhidwa anga adzasangalala nthawi zambiri ndi nchito za manja ao.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 65

Onani Yesaya 65:22 nkhani