Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 65:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Taonani atumiki anga adzadya, koma inu mudzakhala ndi njala; taonani, atumiki anga adzamwa, koma inu mudzakhala ndi ludzu; taonani, atumiki anga adzasangalala, koma inu mudzakhala ndi manyazi;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 65

Onani Yesaya 65:13 nkhani