Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 65:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndidzasankhiratu inu kulupanga, ndipo inu nonse mudzagwada ndi kuphedwa; pakuti pamene ndinaitana, inu simunayankhe; pamene ndinanena, simunamve; koma munacita coipa m'maso mwanga, ndi kusankha cimene Ine sindinakondwera naco.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 65

Onani Yesaya 65:12 nkhani