Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 64:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inu mukomana ndi iye amene akondwerera, nacita cilungamo, iwo amene akumbukira Inu m'njira zanu; taonani Inu munakwiya, ndipo ife tinacimwa; takhala momwemo nthawi yambiri, kodi tidzapulumutsidwa?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 64

Onani Yesaya 64:5 nkhani