Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 60:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Gulu la ngamila lidzakukuta, ngamila zazing'ono za Midyani ndi Efa; iwo onsewo adzacokera ku Seba adzabwera nazo golidi ndi zonunkhira; ndipo adzalalikira matamando a Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 60

Onani Yesaya 60:6 nkhani