Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 60:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo alendo adzamanga malinga ako, ndi mafumu ao adzakutumikira; pakuti m'kukwiya kwanga ndinakantha, koma mokomera mtima ndidakucitira iwe cifundo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 60

Onani Yesaya 60:10 nkhani