Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 59:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunena za. Ine, ili ndi pangano langa ndi iwo, ati Yehova; mzimu wanga umene uli pa iwe, ndi mau anga amene ndaika m'kamwa mwako sadzacoka m'kamwa mwako, pena m'kamwa mwa ana ako, pena m'kamwa mwa mbeu ya mbeu yako, ati Yehova, kuyambira tsopano ndi ku nthawi zonse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 59

Onani Yesaya 59:21 nkhani