Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 59:20-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Ndipo Mombolo adzafika ku Ziyoni, ndi kwa iwo amene atembenuka kusiya kulakwa mwa Yakobo, ati Yehova.

21. Ndipo kunena za. Ine, ili ndi pangano langa ndi iwo, ati Yehova; mzimu wanga umene uli pa iwe, ndi mau anga amene ndaika m'kamwa mwako sadzacoka m'kamwa mwako, pena m'kamwa mwa ana ako, pena m'kamwa mwa mbeu ya mbeu yako, ati Yehova, kuyambira tsopano ndi ku nthawi zonse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 59