Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 59:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anabvala cilungamo monga cida ca pacifuwa, ndi cisoti ca cipulumutso pamutu pace; nabvala zobvala zakubwezera cilango, nabvekedwa ndi cangu monga copfunda,

Werengani mutu wathunthu Yesaya 59

Onani Yesaya 59:17 nkhani