Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 57:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo unanka kwa mfumu, utadzola mafuta ndi kucurukitsa zonunkhira zako; ndipo unatumiza atumwi ako kutari; ndipo wadzicepetsa wekha kufikira kunsi ku manda.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 57

Onani Yesaya 57:9 nkhani